Salimo 39:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumtima mwanga munayaka moto.* Ndili mkati moganizira,* moto unapitiriza kuyaka. Kenako ndinanena kuti:
3 Mumtima mwanga munayaka moto.* Ndili mkati moganizira,* moto unapitiriza kuyaka. Kenako ndinanena kuti: