Salimo 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zoonadi, moyo wa munthu aliyense umangodutsa ngati chithunzithunzi. Iye amangovutika* popanda phindu. Amaunjika chuma, osadziwa kuti amene adzasangalale nacho ndi ndani.+
6 Zoonadi, moyo wa munthu aliyense umangodutsa ngati chithunzithunzi. Iye amangovutika* popanda phindu. Amaunjika chuma, osadziwa kuti amene adzasangalale nacho ndi ndani.+