Salimo 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,*Ndipo iye anatchera khutu* kwa ine nʼkumva kulira kwanga kopempha thandizo.+
40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,*Ndipo iye anatchera khutu* kwa ine nʼkumva kulira kwanga kopempha thandizo.+