Salimo 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sindibisa chilungamo chanu mumtima mwanga. Ndimalengeza kuti ndinu wokhulupirika komanso kuti mumapulumutsa atumiki anu. Sindibisa chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu mumpingo waukulu.”+
10 Sindibisa chilungamo chanu mumtima mwanga. Ndimalengeza kuti ndinu wokhulupirika komanso kuti mumapulumutsa atumiki anu. Sindibisa chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu mumpingo waukulu.”+