Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundisonyeza chifundo. Chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu zizinditeteza nthawi zonse.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:11 Nsanja ya Olonda,6/1/2005, ptsa. 9, 11-12
11 Inu Yehova, musasiye kundisonyeza chifundo. Chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu zizinditeteza nthawi zonse.+