-
Salimo 41:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mmodzi wa iwo akabwera kudzandiona, sanena zinthu moona mtima.
Amasonkhanitsa nkhani zoipa.
Akatero amachoka nʼkukafalitsa nkhani zoipazo.
-