Salimo 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ine mumandithandiza chifukwa choti ndine wokhulupirika,+Ndipo mudzasangalala nane mpaka kalekale.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:12 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 69/15/2008, tsa. 5
12 Koma ine mumandithandiza chifukwa choti ndine wokhulupirika,+Ndipo mudzasangalala nane mpaka kalekale.*+