Salimo 42:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chiyani ndataya mtima?+ Nʼchifukwa chiyani ndikuvutika mumtima mwanga? Ndidzayembekezera Mulungu,+Ndidzamutamanda chifukwa iye ndi Mpulumutsi wanga Wamkulu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:5 Nsanja ya Olonda,1/15/1995, tsa. 19
5 Nʼchifukwa chiyani ndataya mtima?+ Nʼchifukwa chiyani ndikuvutika mumtima mwanga? Ndidzayembekezera Mulungu,+Ndidzamutamanda chifukwa iye ndi Mpulumutsi wanga Wamkulu.+