Salimo 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zonsezi zatigwera, koma sitinakuiwaleni,Ndipo sitinaphwanye pangano lanu.+