Salimo 44:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nyamukani kuti mutithandize+ Tipulumutseni* chifukwa cha chikondi chanu chokhulupirika.+