Salimo 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aakazi a mafumu ali mʼgulu la akazi amene umawalemekeza. Mkazi wamkulu wa mfumu waima* kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:9 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 9
9 Ana aakazi a mafumu ali mʼgulu la akazi amene umawalemekeza. Mkazi wamkulu wa mfumu waima* kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+