Salimo 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Adzamubweretsa kwa mfumu atavala zovala zokongola.* Anamwali anzake omuperekeza akuwabweretsa kwa iwe. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:14 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, ptsa. 10, 11-126/1/2006, ptsa. 8-9
14 Adzamubweretsa kwa mfumu atavala zovala zokongola.* Anamwali anzake omuperekeza akuwabweretsa kwa iwe.