Salimo 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuthetsa nkhondo padziko lonse lapansi.+ Wathyola uta ndi kupindapinda mkondo.Ndipo wawotcha pamoto magaleta ankhondo.* Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 189 Nsanja ya Olonda,1/1/2004, tsa. 54/15/1990, tsa. 5
9 Akuthetsa nkhondo padziko lonse lapansi.+ Wathyola uta ndi kupindapinda mkondo.Ndipo wawotcha pamoto magaleta ankhondo.*