Salimo 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndi malo athu othawirako otetezeka.+ (Selah)
11 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndi malo athu othawirako otetezeka.+ (Selah)