Salimo 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu wakhala Mfumu ya mitundu ya anthu.+ Mulungu wakhala pampando wake wachifumu wopatulika.