Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:2 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 20
2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+