Salimo 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munsanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,Mulungu wasonyeza kuti iye ndi malo othawirako otetezeka.*+
3 Munsanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,Mulungu wasonyeza kuti iye ndi malo othawirako otetezeka.*+