Salimo 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zimene tinangomva, tsopano taziona tokha,Mumzinda wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mumzinda wa Mulungu wathu. Mulungu adzakhazikitsa mzindawo mpaka kalekale.+ (Selah)
8 Zimene tinangomva, tsopano taziona tokha,Mumzinda wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mumzinda wa Mulungu wathu. Mulungu adzakhazikitsa mzindawo mpaka kalekale.+ (Selah)