Salimo 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sindidzachita mantha pa nthawi yamavuto,+Pamene anthu oipa andizungulira kuti andivulaze.