Salimo 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzafa ngati nkhosa zimene zikupita kokaphedwa. Imfa idzakhala mʼbusa wawo.Mʼmawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+ Matupi awo adzawonongeka.+Kwawo kudzakhala ku Manda*+ osati mʼnyumba yachifumu.+
14 Iwo adzafa ngati nkhosa zimene zikupita kokaphedwa. Imfa idzakhala mʼbusa wawo.Mʼmawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+ Matupi awo adzawonongeka.+Kwawo kudzakhala ku Manda*+ osati mʼnyumba yachifumu.+