Salimo 50:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Yehova, Mulungu wa milungu+ walankhula.Iye akuitana anthu onse okhala padziko lapansi,Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.*
50 Yehova, Mulungu wa milungu+ walankhula.Iye akuitana anthu onse okhala padziko lapansi,Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.*