Salimo 50:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sangakhale chete.+ Pamaso pake pali moto wowononga,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali chimphepo chamkuntho.+
3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sangakhale chete.+ Pamaso pake pali moto wowononga,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali chimphepo chamkuntho.+