Salimo 50:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yamikani Mulungu kuti ikhale ngati nsembe imene mukupereka kwa iye,+Ndipo perekani kwa Wamʼmwambamwamba zimene mwalonjeza.+
14 Yamikani Mulungu kuti ikhale ngati nsembe imene mukupereka kwa iye,+Ndipo perekani kwa Wamʼmwambamwamba zimene mwalonjeza.+