Salimo 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Utachita zinthu zimenezi, ine sindinalankhule kanthu,Choncho unkaganiza kuti ndikuona zinthu ngati mmene iweyo ukuzionera. Koma tsopano ndikudzudzulaNdipo ndikuuza mlandu umene ndakupeza nawo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:21 Nsanja ya Olonda,10/15/2010, ptsa. 3-4
21 Utachita zinthu zimenezi, ine sindinalankhule kanthu,Choncho unkaganiza kuti ndikuona zinthu ngati mmene iweyo ukuzionera. Koma tsopano ndikudzudzulaNdipo ndikuuza mlandu umene ndakupeza nawo.+