Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:1 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 10
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+