Salimo 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Nʼchifukwa chiyani ukudzitukumula chifukwa cha zinthu zoipa zimene ukuchita, wamphamvu iwe?+ Chikondi chokhulupirika cha Mulungu nʼchokhalitsa.+
52 Nʼchifukwa chiyani ukudzitukumula chifukwa cha zinthu zoipa zimene ukuchita, wamphamvu iwe?+ Chikondi chokhulupirika cha Mulungu nʼchokhalitsa.+