Salimo 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ine ndidzakhala ngati mtengo waukulu wa maolivi wa masamba obiriwira mʼnyumba ya Mulungu.Ndidzadalira chikondi chokhulupirika cha Mulungu+ mpaka kalekale. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:8 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 117/1/2005, ptsa. 13-145/15/2000, tsa. 2910/15/1986, tsa. 29
8 Koma ine ndidzakhala ngati mtengo waukulu wa maolivi wa masamba obiriwira mʼnyumba ya Mulungu.Ndidzadalira chikondi chokhulupirika cha Mulungu+ mpaka kalekale.