Salimo 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita zopanda chilungamo za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 53:1 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 1010/1/1997, ptsa. 6-7
53 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita zopanda chilungamo za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+