Salimo 53:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma kuchokera kumwamba, Mulungu amayangʼana ana a anthu,+Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, ngati pali aliyense amene akufunafuna Yehova.+
2 Koma kuchokera kumwamba, Mulungu amayangʼana ana a anthu,+Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, ngati pali aliyense amene akufunafuna Yehova.+