Salimo 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma adzagwidwa ndi mantha aakulu,Mantha amene sanayambe agwidwapo chiyambire,*Chifukwa Mulungu adzamwaza mafupa a anthu amene akukuukirani.* Mudzawachititsa manyazi chifukwa Yehova wawakana.
5 Koma adzagwidwa ndi mantha aakulu,Mantha amene sanayambe agwidwapo chiyambire,*Chifukwa Mulungu adzamwaza mafupa a anthu amene akukuukirani.* Mudzawachititsa manyazi chifukwa Yehova wawakana.