-
Salimo 55:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Nthawi zonse ndimanena kuti: “Ndikanakhala ndi mapiko ngati njiwa!
Ndikanaulukira kutali nʼkukakhala malo otetezeka.
-