Salimo 55:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu adzamva ndipo adzawapatsa chilango,+Amene wakhala pampando wachifumu kuyambira kalekale.+ (Selah) Iwo adzakana kusintha,Anthu amene sanaope Mulungu.+
19 Mulungu adzamva ndipo adzawapatsa chilango,+Amene wakhala pampando wachifumu kuyambira kalekale.+ (Selah) Iwo adzakana kusintha,Anthu amene sanaope Mulungu.+