Salimo 56:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndikomereni mtima inu Mulungu, chifukwa anthu akundiukira.* Tsiku lonse amamenyana nane ndi kundipondereza.
56 Ndikomereni mtima inu Mulungu, chifukwa anthu akundiukira.* Tsiku lonse amamenyana nane ndi kundipondereza.