Salimo 56:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimadalira Mulungu, ndimamutamanda chifukwa cha mawu ake.Ine ndimadalira Mulungu, sindikuopa. Kodi munthu wamba angandichite chiyani?+
4 Ndimadalira Mulungu, ndimamutamanda chifukwa cha mawu ake.Ine ndimadalira Mulungu, sindikuopa. Kodi munthu wamba angandichite chiyani?+