Salimo 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku limene ndidzapemphe kuti mundithandize, adani anga adzathawa.+ Mulungu ali kumbali yanga. Sindikukaikira zimenezi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2024, tsa. 6
9 Pa tsiku limene ndidzapemphe kuti mundithandize, adani anga adzathawa.+ Mulungu ali kumbali yanga. Sindikukaikira zimenezi.+