-
Salimo 56:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndimadalira Mulungu, ndimamutamanda chifukwa cha mawu ake.
Ndimadalira Yehova, ndimamutamanda chifukwa cha mawu ake.
-