Salimo 56:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndimadalira Mulungu. Sindikuopa.+ Kodi munthu wamba angandichite chiyani?+