Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:1 Nsanja ya Olonda,2/1/1986, tsa. 16
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+