Salimo 57:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dzuka, iwe ulemerero wanga. Dzuka, iwe choimbira cha zingwe, ndi iwenso zeze. Ine ndidzadzuka mʼbandakucha.+
8 Dzuka, iwe ulemerero wanga. Dzuka, iwe choimbira cha zingwe, ndi iwenso zeze. Ine ndidzadzuka mʼbandakucha.+