Salimo 58:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Oipa amasochera* akangobadwa.*Iwo amakhala osamvera komanso abodza kuchokera nthawi imene anabadwa. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:3 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 10
3 Oipa amasochera* akangobadwa.*Iwo amakhala osamvera komanso abodza kuchokera nthawi imene anabadwa.