Salimo 58:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu, agululeni mano mʼkamwa mwawo. Inu Yehova, thyolani nsagwada za mikango* imeneyi.