Salimo 59:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa inu Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, ndinu Mulungu wa Isiraeli.+ Nyamukani ndipo muone zimene mitundu yonse ya anthu ikuchita. Musasonyeze chifundo kwa aliyense woipa komanso wachiwembu.+ (Selah)
5 Chifukwa inu Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, ndinu Mulungu wa Isiraeli.+ Nyamukani ndipo muone zimene mitundu yonse ya anthu ikuchita. Musasonyeze chifundo kwa aliyense woipa komanso wachiwembu.+ (Selah)