Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tamverani zimene zikutuluka pakamwa pawo.Milomo yawo ili ngati malupanga,+Chifukwa iwo akuti: “Ndani akumvetsera?”+
7 Tamverani zimene zikutuluka pakamwa pawo.Milomo yawo ili ngati malupanga,+Chifukwa iwo akuti: “Ndani akumvetsera?”+