Salimo 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha tchimo lapakamwa pawo ndi mawu a milomo yawo,Ndiponso chifukwa cha mawu otukwana komanso achinyengo amene amalankhula,+ Akodwe ndi kunyada kwawoko.
12 Chifukwa cha tchimo lapakamwa pawo ndi mawu a milomo yawo,Ndiponso chifukwa cha mawu otukwana komanso achinyengo amene amalankhula,+ Akodwe ndi kunyada kwawoko.