Salimo 59:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muwawononge onse mutakwiya.+Muwawononge kuti asakhaleponso.Muwadziwitse kuti Mulungu akulamulira mbadwa za Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ (Selah)
13 Muwawononge onse mutakwiya.+Muwawononge kuti asakhaleponso.Muwadziwitse kuti Mulungu akulamulira mbadwa za Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ (Selah)