Salimo 60:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Perekani* chizindikiro kwa anthu amene amakuopaniKuti athawe ndi kuzemba uta. (Selah)