Salimo 62:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi mudzamenya munthu kuti mumuphe mpaka liti?+ Nonsenu ndinu oopsa ngati khoma lopendekeka, khoma lamiyala limene latsala pangʼono kugwa.
3 Kodi mudzamenya munthu kuti mumuphe mpaka liti?+ Nonsenu ndinu oopsa ngati khoma lopendekeka, khoma lamiyala limene latsala pangʼono kugwa.