Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,Kapena kudalira uchifwamba. Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu usakhale pachumacho.+
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,Kapena kudalira uchifwamba. Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu usakhale pachumacho.+