Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+ Ine ndikulakalaka inu.*+ Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inuMʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+ Ine ndikulakalaka inu.*+ Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inuMʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+