Salimo 64:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Inu Mulungu, imvani mawu anga pamene ndikukuchondererani.+ Tetezani moyo wanga ku zinthu zoopsa zimene mdani akuchita.
64 Inu Mulungu, imvani mawu anga pamene ndikukuchondererani.+ Tetezani moyo wanga ku zinthu zoopsa zimene mdani akuchita.